Machitidwe a Zipembedzo Zonyenga: Gawo lachiwiri

July 29, 2024

Mupologamuyi, a Kennedy Gondwe ochokera ku Centers for Apologetics Research (CFAR) akupitiliza kulongosora za maonekedwe a mipingo yabodza. Iwo akuti mipingo yabodza imachulukitsa ndi kugawa. Koma kodi imachulukitsa ndi kugawa chani?