Mpingo wa Seventh-day Adventist: Gawo lachiwiri

July 30, 2024

Kodi a Seventh-day Adventist ndi mpingo owona? A Kennedy Gondwe akolongosora kuti ngati bungwe, a Seventh-day Adventist simpingo owona. Iwo akunena kuti izi zilichomwechi chifukwa choti iwo amaphunzitsa ziphunzitso zabodza. Mupogologamuyi iwo akulongosora ziphunzitso zabodzazi.