Mpingo wa Seventh-day Adventist: Gawo loyamba

July 29, 2024

Mpingo wa Seventh-day Adventist ndi umodzi wa mipingo kumwera kwa Africa yomwe ikukula kwambiri. Mipingo yambiri imautenga mpingowu ngati wachibale. Koma kodi mpingowu tiutenge ngati owona? A Kennedy Gondwe ochokera ku Centers for Apologetics Research (CFAR) akuyankha mafunsowa mupologamuyi. Iwo akulongosoranso za mbiri ya Seventh-day Adventist.